Yoswa 23:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndakugawirani mitundu ya anthu iyi yotsala ikhale colowa ca mapfuko anu, kuyambira ku Yordano, ndi mitundu yonse ya anthu ndinaipasula, mpaka ku nyanja yaikuru ku malowero a dzuwa.

Yoswa 23

Yoswa 23:1-12