Yoswa 21:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana a Merari, monga mwa mabanja ao, analandira motapa pa pfuko la Rubeni, ndi pa pfuko la Gadi, ndi pa pfuko la Zebuloni midzi khumi ndi iwiri.

Yoswa 21

Yoswa 21:5-11