Yoswa 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Gerisoni analandira molota maere motapa pa mabanja a pfuko la Isakara, ndi pa pfuko la Aseri, ndi pa pfuko la Nafitali, ndi pa pfuko la Manase logawika pakati m'Basana, midzi khumi ndi itatu.

Yoswa 21

Yoswa 21:5-7