Yoswa 21:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sikadasowa kanthu konse ka zinthu zokoma zonse Yehova adazinenera nyumba ya Israyeli; zidacitika zonse.

Yoswa 21

Yoswa 21:42-45