Yoswa 21:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anawapatsa mpumulo pozungulira ponse, monga mwa zonse adalumbirira makolo ao; ndipo pamaso pao sipanaima munthu mmodzi wa adani ao onse; Yehova anapereka adani ao onse m'manja mwao.

Yoswa 21

Yoswa 21:35-45