Yoswa 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati iye, Momwemo, monga mwa mau anu. Ndipo anawauza amuke, iwo namuka; namanga iye cingwe cofiiraco pazenera.

Yoswa 2

Yoswa 2:12-24