Yoswa 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, mundilumbiriretu kwa Yehova, popeza ndakucitirani cifundo, kuti inunso mudzacitira cifundo a m'nyumba ya atate wanga ndi kundipatsa cizindikilo coona,

Yoswa 2

Yoswa 2:2-14