Yoswa 2:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo titamva ici mitima yathu inasungunuka; anahbenso mtima ndi mmodzi yense, cifukwa ca inu; pakuti Yehova Mulungu wanu, ndiye Mulungu wa m'mwamba umo, ndi pa dziko lapansi.

Yoswa 2

Yoswa 2:7-18