Yoswa 11:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo kunali, pamene Yabini mfumu ya ku Hazoro anacimva, anatwna kwa Yabobu mfumu ya ku Madoni, ndi kwa mfumu ya ku Simironi, ndi kwa mfumu ya ku Akasafu,

2. ndi kwa mafwnu akukhala kumpoto kumapiri, ndi kucigwa kwumwela kwa Kineroto, ndi kucidikha, ndi ku mitunda ya Doro kwnadzulo;

Yoswa 11