Yoswa 10:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

napereka Yehova Lakisi m'dzanja la Israyeli, ndipo anaulanda tsiku laciwiri, naukantha ndi lupanga lakuthwa, ndi amoyo onse anali m'mwemo monga mwa zonse anacitira Libina.

Yoswa 10

Yoswa 10:22-40