Yoswa 10:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa, ndi Aisrayeli onse naye, anapitirira kucokera ku Libina kumka ku Lakisi; namanga misasa, nathira nkhondo pa uwo;

Yoswa 10

Yoswa 10:26-32