Yona 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo amarinyero anacita mantha, napfuulira yense kwa mlungu wace, naponya m'nyanja akatundu anali m'combo kucipepuza. Koma Yona adatsikira m'munsi mwa combo, nagona tulo tofa nato.

Yona 1

Yona 1:1-10