Yona 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova anautsa cimphepo cacikuru panyanja, ndipo panali namondwe wamkuru panyanja, ndi combo cikadasweka.

Yona 1

Yona 1:1-7