Yohane 6:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti cifuniro ca Atate wanga ndi ici, kuti yense wakuyang'ana Mwana, ndi kukhulupirira iye, akhale nao moyo wosatha; ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomariza.

Yohane 6

Yohane 6:37-42