Yohane 6:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cifuniro ca Iye amene anandituma Ine ndi ici, kuti za ici conse Iye anandipatsa Ine ndisatayeko kanthu, koma ndiciukitse tsiku lomariza.

Yohane 6

Yohane 6:35-40