Yohane 6:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gwirani nchito si cifukwa ca cakudya cimene citayika koma ca cakudya cimene citsalira ku moyo wosatha, cimene Mwana wa munthu adzakupatsani inu; pakuti ameneyo Atate, ndiye Mulungu, adamlembera cizindikilo.

Yohane 6

Yohane 6:24-29