Yohane 6:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu anayankha iwo nati, Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Mundifuna Ine, si cifukwa munaona zizindikilo, koma cifukwa munadya mkate, nimunakhuta.

Yohane 6

Yohane 6:23-36