Yohane 4:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi simunena inu, kuti, Yatsala miyezi inai, ndipo kudza kumweta? Onani ndinena kwa inu, Kwezani maso anu, nimuyang'ane m'minda, kuti mwayera kale kufikira kumweta.

Yohane 4

Yohane 4:31-37