Yohane 4:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena nao, Cakudya canga ndico kuti ndicite cifuniro ca iye amene anandituma Ine, ndi kutsiriza nchito yace.

Yohane 4

Yohane 4:25-43