Yohane 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene mkuluyo analawa madzi osanduka vinyowo, ndipo sanadziwa kumene anacokera (koma atumiki amene adatiinga madzi anadziwa), mkuluyo anaitana mkwati,

Yohane 2

Yohane 2:2-12