Yohane 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nanena naye, Munthu ali yense amayamba kuika vinyo wokoma; ndipo anthu atamwatu, pamenepo wina wosakoma; koma iwe wasunga vinyo wokoma kufikira tsopano lino.

Yohane 2

Yohane 2:1-14