Yohane 19:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Pilato, m'mene adamva mau awa, anaturuka ndi Yesu, nakhala pansi pa mpando woweruzira kumalo dzina lace; Bwalo lamiyala, koma m'Cihebri, Gabata,

Yohane 19

Yohane 19:10-21