Yohane 19:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pa ici Pilato anafuna kumasula iye; koma Ayuda anapfuula, ndi kunena, Ngati mumasula ameneyo, simuli bwenzi la Kaisara; yense wodziyesera yekha mfumu atsutsana naye Kaisara.

Yohane 19

Yohane 19:5-19