Yohane 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena naye, Kodi ndiri ndiinu nthawi yaikuru yotere, ndipo sunandizindikira, Filipo? iye amene wandiona Ine waona Atate; unena iwe bwanji, Mutionetsere Atate?

Yohane 14

Yohane 14:1-16