Yohane 14:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sukhulupirira kodi kuti ndiri Ine mwa Atate, ndi Atate ali mwa Ine? Mau amene ndinena Ine kwa inu sindilankhula kwa Ine ndekha; koma Atate wokhala mwa Ine acita nchito zace.

Yohane 14

Yohane 14:1-20