Yohane 11:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Mariya, pofika pamene panali Yesu, m'mene anamuona iye, anagwa pa mapazi ace, nanena ndi iye, Ambuye, mukadakhala kuno Inu, mlongo wanga sakadamwalira.

Yohane 11

Yohane 11:31-34