Yohane 11:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Ayuda okhala naye m'nyumba, ndi kumtonthoza iye, pakuona Mariya ananyamuka msanga, naturuka, namtsata iye, ndi kuyesa kuti amuka kumanda kukalira komweko.

Yohane 11

Yohane 11:23-38