Yohane 1:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesu anaceuka, napenya iwo alikumtsata, nanena nao, Mufuna ciani? Ndipo anati kwa iye, Rabi (ndiko kunena posandulika, Mphunzitsi), mukhala kuti?

Yohane 1

Yohane 1:28-45