Yohane 1:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mau anasandulika thupi, nakhazikika pakati pa ife, ndipo tinaona ulemerero wace, ulemerero wonga wa wobadwa yekha wa Atate, wodzala ndi cisomo ndi coonadi.

Yohane 1

Yohane 1:7-20