Yobu 9:32-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pakuti sindiye munthu, monga ine, kuti ndimyankhe,Kuti tikomane mlandu. Palibe wakutiweruza,Wakutisanjika ife tonse