Yobu 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtima wanga ulema nao moyo wanga,Ndidzadzilolera kudandaula kwanga,Ndidzalankhula pakuwawa mtima wanga.

Yobu 10

Yobu 10:1-6