Yobu 9:10-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Wocita zazikuru zosasanthulika,Ndi zodabwiza zosawerengeka,

11. Taona, Mulungu apita pali ine, koma sindimpenya;Napitirira, koma osamaindikira ine.

12. Taona, akwatula, adzambwezetsa ndani?Adzanena naye ndani, Mulikucita ciani?

Yobu 9