Yobu 9:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pamenepo Yobu anayankha, nati, Zoona, ndidziwa kuti ciri cotero.Koma munthu adzakhala walungama bwanji kwa Mulungu?