Yobu 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Satana, Kodi waonerera mtumiki wanga Yobu? pakuti palibe wina wonga iye m'dzikomo, munthu wangwiro ndi woongoka, wakuopa Mulungu ndi kupewa zoipa.

Yobu 1

Yobu 1:1-17