Yobu 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Yehova kwa Satana, Ufuma kuti? Nayankha Satana kwa Yehova, nati, Kupitapita m'dziko ndi kuyendayenda m'mwemo.

Yobu 1

Yobu 1:1-11