Yesaya 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa ine, tiri zizindikilo ndi zodabwitsa mwa Israyeli, kucokera kwa Yehova wa makamu, amene akhala m'phiri la Ziyoni.

Yesaya 8

Yesaya 8:14-22