Yesaya 66:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala kuti kuyambira pa mwezi wokhala kufikira ku unzace, ndi kuyambira pa Sabata lina kufikira ku linzace, anthu onse adzafika kudzapembedzera pamaso pa Ine, ati Yehova.

Yesaya 66

Yesaya 66:14-24