Yesaya 66:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti monga m'mwamba mwatsopano ndi dziko lapansi latsopano limene ndidzalenga, lidzakhalabe pamaso pa Ine, ati Yehova, momwemo adzakhalabe ana anu ndi dzina lanu.

Yesaya 66

Yesaya 66:15-24