Yesaya 66:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ine ndidziwa nchito zao ndi maganizo ao; nthawi ikudza yakudzasonkhanitsa Ine a mitundu yonse ndi zinenedwe zonse, ndipo adzafika nadzaona ulemerero wanga.

Yesaya 66

Yesaya 66:14-19