Yesaya 66:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo amene adzipatulitsa nadziyeretsa, kuti amuke kuminda tsatane tsatane, ndi kudya nyama ya nkhumba, ndi conyansa, ndi mbewa, adzathedwa pamodzi, ati Yehova.

Yesaya 66

Yesaya 66:10-18