Yesaya 65:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaturutsa mbeu mwa Yakobo, ndi mwa Yuda wolowa nyumba wa mapiri anga; ndipo osankhidwa anga adzalandira colowa cao, ndi atumiki anga adzakhala kumeneko.

Yesaya 65

Yesaya 65:2-11