Yesaya 65:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Monga vinyo watsopano apezedwa m'tsango, ndipo wina ati, Usaliononge, pakuti muli mdalitso m'menemo, momwemo ndidzacita cifukwa ca atumiki anga, kuti ndisawaononge onse.

Yesaya 65

Yesaya 65:3-12