Yesaya 62:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca Ziyoni sindidzakhala cete, ndi cifukwa ca Yerusalemu sindidzapuma, kufikira cilungamo cace cidzaturuka monga kuyera, ndi cipulumutso cace monga nyali yoyaka.

Yesaya 62

Yesaya 62:1-6