Yesaya 61:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti monga dziko liphukitsa mphundu zace, ndi monga munda umeretsa zobzalamo, momwemo Ambuye Yehova adzaphukitsa cilungamo ndi matamando pamaso pa amitundu onse.

Yesaya 61

Yesaya 61:9-11