Yesaya 59:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ciweruziro cabwerera m'mbuyo, ndi cilungamo caima patari; pakuti coona cagwa m'khwalala, ndi kuongoka sikungalowe.

Yesaya 59

Yesaya 59:11-19