Yesaya 59:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndizo kulakwabe ndi kukanabe Yehova, ndi kuleka kutsata Mulungu wathu, kulankhula zotsendereza ndi kupanduka, kuganizira ndi kunena pakamwa mau akunyenga oturuka mumtima.

Yesaya 59

Yesaya 59:11-14