Yesaya 58:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo udzaitana, ndipo Yehova adzayankha; udzapfuula ndipo Iye adzati, Ndine pano. Ngati ucotsa pakati pa iwe gori, kukodolana moipa, ndi kulankhula moipa,

Yesaya 58

Yesaya 58:7-14