Yesaya 58:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ngati upereka kwa wanjala cimene moyo Iwako umakhumba, ndi kukhutitsa moyo wobvutidwa, pomwepo kuunika kwako kudzauka mumdima, ndipo usiku wako udzanga usana;

Yesaya 58

Yesaya 58:6-14