Yesaya 56:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wodala munthu amene acita ici, ndi mwana wa munthu amene agwira zolimba ici, amene asunga sabata osaliipitsa, nasunga dzanja lace osacita nalo coipa ciri conse.

Yesaya 56

Yesaya 56:1-9