Yesaya 51:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Galamuka, galamuka, khala ndi mphamvu, mkono wa Yehova; galamuka monga masiku akale, mibadwo ya nthawi zakale. Kodi si ndiwe amene unadula Rahabu zipinjiri zipinjiri, amene unapyoza cinjoka cija?

Yesaya 51

Yesaya 51:1-10